Genesis 7:14 - Buku Lopatulika14 iwo, ndi zamoyo zonse monga mwa mitundu yao, ndi zinyama zonse monga mwa mitundu yao, zokwawa zonse zokwawa padziko lapansi monga mwa mitundu yao, ndi zouluka zonse monga mwa mitundu yao, ndi mbalame zonse za mitundumitundu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 iwo, ndi zamoyo zonse monga mwa mitundu yao, ndi zinyama zonse monga mwa mitundu yao, zokwawa zonse zokwawa pa dziko lapansi monga mwa mitundu yao, ndi zouluka zonse monga mwa mitundu yao, ndi mbalame zonse za mitundumitundu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Iwowo adaloŵa m'chombo pamodzi ndi mtundu uliwonse wa nyama zakuthengo, zoŵeta, nyama zokwaŵa ndi mbalame za mtundu uliwonse. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Iwowa analowa mʼchombomo pamodzi ndi nyama iliyonse ya kutchire monga mwa mtundu wake, ziweto zonse monga mwa mitundu yawo, nyama yokwawa iliyonse monga mwa mtundu wake ndi mbalame iliyonse monga mwa mtundu wake. Onani mutuwo |