Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 6:15 - Buku Lopatulika

15 Kupanga kwake ndi kotere: m'litali mwake mwa chingalawa mikono mazana atatu, m'mimba mwake mikono makumi asanu, m'msinkhu mwake mikono makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

15 Kupanga kwake ndi kotere: m'litali mwake mwa chingalawa mikono mazana atatu, m'mimba mwake mikono makumi asanu, m'msinkhu mwake mikono makumi atatu.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

15 M'litali mwake mwa chombocho mukhale mamita 140. M'mimba mwake mukhale mamita 23, ndipo msinkhu wake ukhale wa mamita 13 ndi theka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

15 Uchipange motere: Chombo chikhale mamita 140 mulitali, mamita 23 mulifupi ndi mamita 13 mu msinkhu wake.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 6:15
4 Mawu Ofanana  

Udzipangire wekha chingalawa cha mtengo wanjale; upangemo zipinda m'chingalawamo, ndipo upake ndi utoto m'kati ndi kunja.


Uike zenera m'chingalawacho, ulimalize ndi kusiya mkono umodzi pamwamba pake: khomo la chingalawa uike m'mbali mwake; nuchipange ndi nyumba yapansi, ndi yachiwiri, ndi yachitatu.


Madzi anapambana ndithu nakwera mikono khumi ndi isanu: namizidwa mapiri.


(Pakuti Ogi mfumu ya Basani anatsala yekha wa iwo otsalira Arefaimu; taonani, kama wake ndiye kama wachitsulo; sukhala kodi mu Raba wa ana a Amoni? Utali wake mikono isanu ndi inai, kupingasa kwake mikono inai, kuyesa mkono wa munthu).


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa