Genesis 6:14 - Buku Lopatulika14 Udzipangire wekha chingalawa cha mtengo wanjale; upangemo zipinda m'chingalawamo, ndipo upake ndi utoto m'kati ndi kunja. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Udzipangire wekha chingalawa cha mtengo wanjale; upangemo zipinda m'chingalawamo, ndipo upake ndi utoto m'kati ndi kunja. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Udzipangire chombo ndipo uchipange ndi matabwa a mtengo wa mnjale. Upange zipinda m'menemo, ndipo uchimate phula kunja kwake ndi m'kati momwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Tsono udzipangire chombo cha matabwa a mtengo wanjale; mʼkati mwake upange zipinda ndipo upake phula mʼkati ndi kunja. Onani mutuwo |