Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 6:1 - Buku Lopatulika

1 Ndipo panali pamene anthu anayamba kuchuluka padziko, ndi ana aakazi anawabadwira iwo,

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

1 Ndipo panali pamene anthu anayamba kuchuluka padziko, ndi ana akazi anawabadwira iwo,

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

1 Nthaŵi imeneyo anthu anali atayamba kuchuluka pa dziko lonse lapansi, ndipo adabereka ana aakazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

1 Anthu atayamba kuchuluka pa dziko lapansi ndi kubereka ana aakazi,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 6:1
3 Mawu Ofanana  

Mulungu ndipo anadalitsa iwo, ndipo adati kwa iwo, Mubalane, muchuluke, mudzaze dziko lapansi, muligonjetse: mulamulire pansomba za m'nyanja, ndi pambalame za m'mlengalenga, ndi pazamoyo zonse zokwawa padziko lapansi.


Ndipo Nowa anali wa zaka mazana asanu; ndipo Nowa anabala Semu ndi Hamu ndi Yafeti.


kuti ana aamuna a Mulungu anayang'ana ana aakazi a anthu, kuti iwo anali okongola; ndipo anadzitengera okha akazi onse amene anawasankha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa