Genesis 5:32 - Buku Lopatulika32 Ndipo Nowa anali wa zaka mazana asanu; ndipo Nowa anabala Semu ndi Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201432 Ndipo Nowa anali wa zaka mazana asanu; ndipo Nowa anabala Semu ndi Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa32 Nowa ali wa zaka zopitirira 500, adabereka ana aamuna atatu: Semu, Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero32 Pamene Nowa anali ndi zaka 500, anabereka Semu, Hamu ndi Yafeti. Onani mutuwo |