Genesis 5:31 - Buku Lopatulika31 masiku ake onse a Lameki anali zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201431 masiku ake onse a Lameki anali zaka mazana asanu ndi awiri kudza makumi asanu ndi awiri; ndipo anamwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa31 Adamwalira ali wa zaka 777. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero31 Zaka zonse za Lameki zinali 777, ndipo kenaka anamwalira. Onani mutuwo |