Genesis 5:30 - Buku Lopatulika30 ndipo Lameki anakhala ndi moyo atabala Nowa, zaka mazana asanu kudza makumi asanu ndi anai ndi zisanu, nabala ana aamuna ndi aakazi: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201430 ndipo Lameki anakhala ndi moyo atabala Nowa, zaka mazana asanu kudza makumi asanu ndi anai ndi zisanu, nabala ana aamuna ndi aakazi: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa30 Lameki adakhalanso ndi moyo zaka zina 595. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero30 Atabadwa Nowa, Lameki anakhala zaka zina 595 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |