Genesis 50:14 - Buku Lopatulika14 Ndipo ataika atate wake, Yosefe anabwera ku Ejipito, iye ndi abale ake, ndi onse amene anakwera pamodzi naye kukaika atate wake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Ndipo ataika atate wake, Yosefe anabwera ku Ejipito, iye ndi abale ake, ndi onse amene anakwera pamodzi naye kukaika atate wake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Yosefe ataika bambo wake m'manda, adabwerera ku Ejipito ndi abale ake aja, pamodzi ndi onse amene adamperekeza. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Atatha kuyika abambo ake, Yosefe anabwerera ku Igupto, pamodzi ndi abale ake ndi onse amene anapita nawo kukayika abambo ake. Onani mutuwo |