Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 50:12 - Buku Lopatulika

12 Ndipo ana ake aamuna anamchitira iye monga anawalamulira iwo;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Ndipo ana ake amuna anamchitira iye monga anawalamulira iwo;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Ana a Yakobe adachitadi monga momwe bambo wao adaaŵalamulira.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Choncho ana a Yakobo anachita monga momwe abambo awo anawalamula:

Onani mutuwo Koperani




Genesis 50:12
7 Mawu Ofanana  

Ndipo pamene anthu okhala m'dzikomo, Akanani, anaona maliro a m'dwale la Atadi, anati, Awa ndi maliro aakulu a Aejipito: chifukwa chake dzina la pamenepo linatchedwa Abele-Mizraimu, pali tsidya lija la Yordani.


chifukwa kuti ana ake aamuna anamnyamula iye kulowa naye m'dziko la Kanani, ndi kumuika iye m'phanga la munda wa Makipela, limene Abrahamu analigula pamodzi ndi munda, likhale poikira pake, kwa Efuroni Muhiti, patsogolo pa Mamure.


Uzilemekeza atate wako ndi amai ako; kuti achuluke masiku ako m'dziko limene Yehova Mulungu wako akupatsa iwe.


ndipo anawanyamula kupita nao ku Sekemu, nawaika m'manda amene Abrahamu adagula ndi mtengo wake wa ndalama kwa ana a Hamori mu Sekemu.


Ananu, mverani akukubalani mwa Ambuye, pakuti ichi nchabwino.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa