Genesis 5:9 - Buku Lopatulika9 Ndipo Enosi anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi anai, nabala Kenani; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Ndipo Enosi anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi anai, nabala Kenani; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Enosi ali wa zaka 90, adabereka mwana dzina lake Kenani, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Pamene Enosi anali ndi zaka 90, anabereka Kenani. Onani mutuwo |