Genesis 5:8 - Buku Lopatulika8 masiku ake onse a Seti anali zaka mazana asanu ndi anai kudza khumi ndi ziwiri; ndipo anamwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 masiku ake onse a Seti anali zaka mazana asanu ndi anai kudza khumi ndi ziwiri; ndipo anamwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 Adamwalira ali wa zaka 912. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 Zaka zonse za Seti zinali 912 ndipo anamwalira. Onani mutuwo |