Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti

- Zotsatsa -




Genesis 5:9 - Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

9 Pamene Enosi anali ndi zaka 90, anabereka Kenani.

Onani mutuwo Koperani

Buku Lopatulika

9 Ndipo Enosi anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi anai, nabala Kenani;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

9 Ndipo Enosi anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi anai, nabala Kenani;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

9 Enosi ali wa zaka 90, adabereka mwana dzina lake Kenani,

Onani mutuwo Koperani




Genesis 5:9
4 Mawu Ofanana  

Atabadwa Kenani, Enosi anakhala ndi moyo zaka zina 815 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.


Zaka zonse za Seti zinali 912 ndipo anamwalira.


Kenani, Mahalaleli, Yaredi,


mwana wa Metusela, mwana wa Enoki, mwana wa Yaredi mwana wa Malaleeli, mwana wa Kainane,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa