Genesis 5:20 - Buku Lopatulika20 masiku ake onse a Yaredi anali zaka mazana asanu ndi anai kudza makumi asanu ndi limodzi ndi ziwiri: ndipo anamwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 masiku ake onse a Yaredi anali zaka mazana asanu ndi anai kudza makumi asanu ndi limodzi ndi ziwiri: ndipo anamwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 Adamwalira ali wa zaka 962. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 Zaka zonse za Yaredi zinali 962 ndipo anamwalira. Onani mutuwo |