Genesis 5:19 - Buku Lopatulika19 ndipo Yaredi anakhala ndi moyo, atabala Enoki, zaka mazana asanu ndi atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 ndipo Yaredi anakhala ndi moyo, atabala Enoki, zaka mazana asanu ndi atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 800. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 Atabadwa Enoki, Yaredi anakhala ndi moyo zaka zina 800 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi. Onani mutuwo |