Genesis 5:21 - Buku Lopatulika21 Ndipo Enoki anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Metusela: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Ndipo Enoki anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Metusela: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 Enoki ali wa zaka 65, adabereka mwana dzina lake Metusela. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 Pamene Enoki anali ndi zaka 65, anabereka Metusela. Onani mutuwo |