Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 5:16 - Buku Lopatulika

16 ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo, atabala Yaredi, zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi:

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

16 ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo, atabala Yaredi, zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi atatu, nabala ana aamuna ndi aakazi:

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

16 ndipo adakhalanso ndi moyo zaka zina 830. Adaberekanso ana ena aamuna ndi aakazi.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

16 Atabadwa Yaredi, Mahalaleli anakhala ndi moyo zaka zina 830 ndipo anabereka ana ena aamuna ndi aakazi.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 5:16
3 Mawu Ofanana  

Ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Yaredi;


masiku ake onse a Mahalalele anali zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi asanu ndi anai ndi zisanu; ndipo anamwalira.


mwana wa Metusela, mwana wa Enoki, mwana wa Yaredi, mwana wa Mahalalele, mwana wa Kainani,


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa