Genesis 5:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Yaredi; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo Mahalalele anakhala ndi moyo zaka makumi asanu ndi limodzi kudza zisanu, nabala Yaredi; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Mahalalele ali wa zaka 65 adabereka Yaredi, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Pamene Mahalaleli anali ndi zaka 65, anabereka Yaredi. Onani mutuwo |