Genesis 5:17 - Buku Lopatulika17 masiku ake onse a Mahalalele anali zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi asanu ndi anai ndi zisanu; ndipo anamwalira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 masiku ake onse a Mahalalele anali zaka mazana asanu ndi atatu kudza makumi asanu ndi anai ndi zisanu; ndipo anamwalira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Adamwalira ali wa zaka 895. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Zaka zonse za Mahalaleli zinali 895 ndipo anamwalira. Onani mutuwo |