Genesis 49:8 - Buku Lopatulika8 Yuda, abale ako adzakuyamika iwe; dzanja lako lidzakhala pa khosi la adani ako; ana aamuna a atate wako adzakuweramira. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20148 Yuda, abale ako adzakuyamika iwe; dzanja lako lidzakhala pa khosi la adani ako; ana amuna a atate wako adzakuweramira. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa8 “Iwe Yuda, abale ako adzakutamanda. Adani ako udzaŵagwira pa khosi, abale ako adzakugwadira iwe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero8 “Yuda, ndiwe amene abale ako adzatamanda; dzanja lako lidzagwira pa khosi pa adani ako; abale ako adzakugwadira iwe. Onani mutuwo |