Genesis 49:6 - Buku Lopatulika6 Mtima wangawe, usalowe mu chiungwe chao; ulemerero wanga, usadziphatike pa msonkhano yao; chifukwa m'kukwiya kwao anapha munthu. M'kufuna kwao anapundula ng'ombe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Mtima wangawe, usalowe mu chiungwe chao; ulemerero wanga, usadziphatike pa masonkhano ao; chifukwa m'kukwiya kwao anapha munthu. M'kufuna kwao anapundula ng'ombe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Ine sindidzakhala nao pa zokambirana zao zam'seri, sindifuna kukhala nao m'misonkhano yao, chifukwa choti adapha anthu mokalipa, ndipo adapundula ng'ombe zamphongo mwankhanza, naziyesa choseketsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iwe moyo wanga, usakhale nawo pa misonkhano yawo ya mseri, kapena kugwirizana nawo mʼmabwalo awo, pakuti anapha anthu mu mkwiyo wawo ndipo anapundula ngʼombe zamphongo monga kunawakomera. Onani mutuwo |