Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 49:5 - Buku Lopatulika

5 Simeoni ndi Levi ndiwo abale; zida za mphulupulu ndizo malupanga ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

5 Simeoni ndi Levi ndiwo abale; zida za mphulupulu ndizo malupanga ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

5 “Simeoni ndi Levi mpachibale pao, amagwiritsa ntchito zida zankhondo pochita chiwawa.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

5 “Simeoni ndi Levi ndi pachibale pawo, anachitira nkhanza anthu amene anachita nawo pangano.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 49:5
8 Mawu Ofanana  

Wogwira ntchito mwaulesi ndiye mbale wake wa wosakaza.


Ndi kumalire a Benjamini, kuyambira mbali ya kum'mawa kufikira mbali ya kumadzulo; Simeoni, gawo limodzi.


Wa fuko la ana a Simeoni, Semuele mwana wa Amihudi.


Motero ana a Israele anapatsa Alevi mizinda iyi ndi mabusa ao, molota maere, monga Yehova adalamulira mwa dzanja la Mose.


Mwa fuko la Simeoni zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko Levi zikwi khumi ndi ziwiri. Mwa fuko la Isakara zikwi khumi ndi ziwiri.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa