Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 49:32 - Buku Lopatulika

32 munda ndi phanga lili m'menemo, zinagulidwa kwa ana a Hiti

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

32 munda ndi phanga lili m'menemo, zinagulidwa kwa ana a Hiti

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

32 Mundawo pamodzi ndi phangalo adagula kwa Ahiti.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

32 Munda ndi manda amene ali mʼmenemo zinagulidwa kwa Ahiti.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 49:32
4 Mawu Ofanana  

Ndipo Kanani anabala Sidoni woyamba wake, ndi Heti,


pamenepo anaika Abrahamu ndi Sara mkazi wake; pamenepo anaika Isaki ndi Rebeka mkazi wake: pamenepo ndinaika Leya:


Pamene Yakobo anatha kulangiza ana ake aamuna, anafunya mapazi ake pakama, natsirizika, nasonkhanitsidwa kwa anthu a mtundu wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa