Genesis 49:21 - Buku Lopatulika21 Nafutali ndi mbawala yomasuka; apatsa mau abwino. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201421 Nafutali ndi mbawala yomasuka; apatsa mau abwino. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa21 “Nafutali ali ngati insa yongoyenda mwaufulu, imene imabala ana okongola. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero21 “Nafutali ali ngati mbawala yayikazi yokhala ndi ana okongola kwambiri. Onani mutuwo |