Genesis 49:20 - Buku Lopatulika20 Ndi Asere, chakudya chake ndicho mafuta, ndipo adzapereka zolongosoka zachifumu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201420 Ndi Asere, chakudya chake ndicho mafuta, ndipo adzapereka zolongosoka zachifumu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa20 “Dziko la Asere lidzabala chakudya chokoma, choyenera kudya mafumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero20 “Dziko la Aseri lidzabereka chakudya chokoma, ndipo iye adzapereka chakudya kwa mafumu. Onani mutuwo |