Genesis 49:19 - Buku Lopatulika19 Ndi Gadi, achifwamba adzampsinja iye; koma iye adzapsinja pa chitendeni chao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201419 Ndi Gadi, achifwamba adzampsinja iye; koma iye adzapsinja pa chitende chao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa19 “Gadi anthu achifwamba adzamthira nkhondo, koma iyeyo adzaŵatembenukira nkuŵapirikitsa. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero19 “Gadi adzachitidwa chiwembu ndi gulu la amaliwongo, koma iye adzawathamangitsa. Onani mutuwo |