Genesis 49:17 - Buku Lopatulika17 Dani adzakhala njoka m'khwalala, songo panjira, imene iluma zitendene za kavalo, kuti womkwera wake agwe chambuyo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201417 Dani adzakhala njoka m'khwalala, songo panjira, imene iluma zitende za kavalo, kuti womkwera wake agwe chambuyo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa17 Dani adzakhala ngati njoka pambali pa mseu, njoka yaululu ndithu m'mbali mwa njira, yoluma ku chidendene cha kavalo, kotero kuti wokwerapo wake adzagwa chagada. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero17 Dani adzakhala ngati njoka ya mʼmphepete mwa msewu, songo yokhala mʼnjira imene imaluma chidendene cha kavalo kuti wokwerapoyo agwe chagada. Onani mutuwo |