Genesis 49:15 - Buku Lopatulika15 Ndipo anaona popumulapo kuti panali pabwino, ndi dziko kuti linali lokondweretsa; ndipo anaweramitsa phewa lake kuti anyamule, nakhala kapolo wakugwira ntchito ya msonkho. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201415 Ndipo anaona popumulapo kuti panali pabwino, ndi dziko kuti linali lokondweretsa; ndipo anaweramitsa phewa lake kuti anyamule, nakhala kapolo wakugwira ntchito ya msonkho. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa15 Ataona kukoma kwa malo ousirapowo, ndi kukongola kwa dzikolo. Adaŵeramitsa msana kuti anyamule katundu wake, ndipo adasanduka womagwira ntchito yaukapolo. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero15 Ataona ubwino wake wa pamalo pake popumira ndi kukongola kwa dziko lake, iye anaweramutsa msana kuti anyamule katundu wake ndipo anasanduka wogwira ntchito ya ukapolo. Onani mutuwo |