Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 49:14 - Buku Lopatulika

14 Isakara ndiye bulu wolimba, alinkugona pakati pa makola.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

14 Isakara ndiye bulu wolimba, alinkugona pakati pa makola.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

14 “Isakara ali ngati bulu wamphamvu, amagona chotambasuka pakati pa makola.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

14 “Isakara ali ngati bulu wamphamvu wogona pansi pakati pa makola.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 49:14
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Leya anati, Mulungu wandipatsa ine mphotho yanga, chifukwa ndapatsa mdzakazi wanga kwa mwamuna wanga: namutcha dzina lake Isakara.


Ndipo anaona popumulapo kuti panali pabwino, ndi dziko kuti linali lokondweretsa; ndipo anaweramitsa phewa lake kuti anyamule, nakhala kapolo wakugwira ntchito ya msonkho.


Ndi a ana a Isakara, anthu akuzindikira nyengo, akudziwa zoyenera Israele kuzichita, akulu ao ndiwo mazana awiri; ndi abale ao onse anapenyerera pakamwa pao.


Pogona inu m'makola a zoweta, mukhala ngati mapiko a njiwa okulira ndi siliva, ndi nthenga zake zokulira ndi golide woyenga wonyezimira.


Ndipo anasankha Davide mtumiki wake, namtenga kumakola a nkhosa.


Ndipo anayandikiza, nati Tidzamangira zoweta zathu makola kuno, ndi ana athu mizinda;


Ndi za Zebuloni anati, Kondwera, Zebuloni, ndi kutuluka kwako; ndi Isakara, m'mahema mwako.


Atafa Abimeleki, anauka kupulumutsa Israele Tola mwana wa Puwa, mwana wa Dodo munthu wa Isakara; nakhala iye mu Samiri ku mapiri a Efuremu.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa