Genesis 49:13 - Buku Lopatulika13 Zebuloni adzakhala m'mphepete mwa nyanja; ndipo iye adzakhala dooko la ngalawa; ndipo malire ake adakhala pa Sidoni. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 Zebuloni adzakhala m'mphepete mwa nyanja; ndipo iye adzakhala dooko la ngalawa; ndipo malire ake adakhala pa Sidoni. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 “Zebuloni adzakhala m'mbali mwa nyanja, madooko ake adzakhala malo a zombo, dziko lake lidzafika mpaka ku Sidoni. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 “Zebuloni adzakhala mʼmphepete mwa nyanja; adzakhala pa dooko la sitima zapamadzi; malire ake adzafika ku Sidoni. Onani mutuwo |