Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 49:12 - Buku Lopatulika

12 Maso ake adzafiira ndi vinyo, ndipo mano ake adzayera ndi mkaka.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

12 Maso ake adzafiira ndi vinyo, ndipo mano ake adzayera ndi mkaka.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

12 Maso ake ndi ofiira ndi vinyo mano ake ndi oyera ndi mkaka.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

12 Maso ake adzakhala akuda chifukwa cha vinyo, mano ake woyera chifukwa cha mkaka.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 49:12
3 Mawu Ofanana  

Adamanga mwana wa kavalo wake pampesa, ndi mwana wa bulu wake pa mpesa wosankhika; natsuka malaya ake m'vinyo, ndi chofunda chake m'mwazi wa mphesa.


Zebuloni adzakhala m'mphepete mwa nyanja; ndipo iye adzakhala dooko la ngalawa; ndipo malire ake adakhala pa Sidoni.


Ndani ali ndi chisoni? Ndani asauka? Ndani ali ndi makangano? Ndani ang'ung'udza? Ndani alasidwa chabe? Ndani afiira maso?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa