Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 47:28 - Buku Lopatulika

28 Ndipo Yakobo anakhala m'dziko la Ejipito zaka khumi mphambu zisanu ndi ziwiri; ndipo masiku a Yakobo zaka za moyo wake zinali zaka zana limodzi mphambu makumi anai kudza zisanu ndi ziwiri.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

28 Ndipo Yakobo anakhala m'dziko la Ejipito zaka khumi mphambu zisanu ndi ziwiri; ndipo masiku a Yakobo zaka za moyo wake zinali zaka zana limodzi mphambu makumi anai kudza zisanu ndi ziwiri.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

28 Yakobe adakhala ku Ejipito, zaka 17, choncho zaka za moyo wake zidakwanira 147.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

28 Yakobo anakhala ku Igupto zaka 17 ndipo zaka za moyo wake zinali 147.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 47:28
7 Mawu Ofanana  

Masiku a zaka za moyo wake wa Abrahamu amene anakhala ndi moyo ndiwo zaka zana limodzi, kudza makumi asanu ndi limodzi, kudza khumi ndi zisanu.


Mibadwo ya Yakobo ndi iyi; Yosefe anali wa zaka khumi ndi zisanu ndi ziwiri analinkudyetsa zoweta pamodzi ndi abale ake; ndipo anali mnyamata pamodzi ndi ana a Biliha, ndi ana aamuna a Zilipa, akazi a atate wake; ndipo Yosefe anamfotokozera atate wake mbiri yao yoipa.


Ana a Pasuri, chikwi chimodzi mphambu mazana awiri kudza makumi anai ndi asanu ndi awiri.


Masiku a mtumiki wanu ndiwo angati? Mudzaweruza liti iwo akundilondola koipa?


Masiku a zaka zathu ndiwo zaka makumi asanu ndi awiri, kapena tikakhala nayo mphamvudi zaka makumi asanu ndi atatu; koma teronso kukula kwao kumati chivuto ndi chopanda pake; pakuti kumapitako msanga ndipo tithawa ife tomwe.


Mutidziwitse kuwerenga masiku athu motero, kuti tikhale nao mtima wanzeru.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa