Genesis 46:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anatenga ng'ombe zao ndi chuma chao anachipeza m'dziko la Kanani, nadza ku Ejipito, Yakobo ndi mbeu zake zonse pamodzi ndi iye; Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anatenga ng'ombe zao ndi chuma chao anachipeza m'dziko la Kanani, nadza ku Ejipito, Yakobo ndi mbeu zake zonse pamodzi ndi iye; Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Adatenga zoŵeta zao zonse pamodzi ndi zinthu zonse zimene anali nazo ku Kanani, ndipo adapita ku Ejipito. Yakobe adatenga zidzukulu zake zonse, Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Iwo anatenganso ziweto zawo ndi katundu wawo amene anali naye ku Kanaani, ndipo Yakobo pamodzi ndi ana ndi zidzukulu zake anapita ku Igupto. Onani mutuwo |