Genesis 45:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo anakwera kutuluka mu Ejipito, nafika ku dziko la Kanani kwa Yakobo atate wao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo anakwera kutuluka m'Ejipito, nafika ku dziko la Kanani kwa Yakobo atate wao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono iwo adachoka ku Ejipito, kubwerera ku Kanani kwa bambo wao Yakobe. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Ndipo anachoka ku Igupto nafika kwa abambo awo Yakobo mʼdziko la Kanaani. Onani mutuwo |