Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 45:24 - Buku Lopatulika

24 Ndipo anamukitsa abale ake, ndipo anachoka; ndipo anati kwa iwo, Musakangane panjira.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

24 Ndipo anamukitsa abale ake, ndipo anachoka; ndipo anati kwa iwo, Musakangane panjira.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

24 Tsono adaŵauza abale akewo kuti azipita, ndipo ponyamukapo adanena kuti, “Musakangane pa njira.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

24 Kenaka anawalola abale ake aja kuti azipita, ndipo akunyamuka, iye anawawuza kuti, “Osakangana mʼnjira!”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 45:24
10 Mawu Ofanana  

Ndipo Rubeni anati kwa iwo, Musakhetse mwazi; mponyeni iye m'dzenjemo m'chipululu muno, koma musamsamulire iye manja: kuti ampulumutse iye m'manja mwao, ambwezenso kwa atate wake.


Kwa atate wake anatumiza zotere: abulu khumi osenza zinthu zabwino za mu Ejipito, ndi abulu aakazi khumi osenza tirigu, ndi chakudya, ndi phoso la atate la panjira.


Ndipo anakwera kutuluka mu Ejipito, nafika ku dziko la Kanani kwa Yakobo atate wao.


ndipo muwachitire ulemu woposatu mwa chikondi, chifukwa cha ntchito yao. Khalani mumtendere mwa inu nokha.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa