Genesis 45:22 - Buku Lopatulika22 Onse anawapatsa yense zovala zopindula; koma Benjamini anampatsa masekeli a siliva mazana atatu ndi zovala zopindula zisanu. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201422 Onse anawapatsa yense zovala zopindula; koma Benjamini anampatsa masekeli a siliva mazana atatu ndi zovala zopindula zisanu. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa22 Adapatsanso aliyense zovala zachikondwerero, koma Benjamini adampatsa mashikeli asiliva okwana 300, ndi zovala zisanu zachikondwerero. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero22 Anaperekanso kwa aliyense zovala zatsopano, koma kwa Benjamini anapereka siliva wolemera pafupifupi makilogalamu anayi ndi zovala zisanu. Onani mutuwo |