Genesis 45:2 - Buku Lopatulika2 Ndipo analira momveka, ndipo anamva Aejipito, ndipo anamva a m'nyumba ya Farao. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Ndipo analira momveka, ndipo anamva Aejipito, ndipo anamva a m'nyumba ya Farao. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Adalira momveka kotero kuti Aejipito adamva ndithu, ndipo mbiri ya zimenezo idakafika mpaka kwa mfumu. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Ndipo analira mokweza mwakuti Aigupto anamva. Onse a ku nyumba kwa Farao anamvanso za zimenezi. Onani mutuwo |