Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 45:17 - Buku Lopatulika

17 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Nena ndi abale ako, Chitani ichi; senzetsani nyama zanu, ndi kupita kunka ku dziko la Kanani;

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

17 Ndipo Farao anati kwa Yosefe, Nena ndi abale ako, Chitani ichi; senzetsani nyama zanu, ndi kupita kunka ku dziko la Kanani;

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

17 Ndipo Farao adauza Yosefe kuti, “Uŵauze abale ako kuti asenzetse nyama zao katundu, ndipo abwerere ku Kanani.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

17 Farao anati kwa Yosefe, “Uwawuze abale ako kuti, ‘Senzetsani nyama zanu katundu ndi kubwerera ku dziko la Kanaani.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 45:17
4 Mawu Ofanana  

Ndipo mbiri yake inamveka m'nyumba ya Farao, kuti abale ake a Yosefe afika; ndipo inamkomera Farao, ndi anyamata ake.


katengeni atate wanu ndi mabanja anu, nimudze kwa ine; ndipo ndidzakupatsani inu zabwino za dziko la Ejipito, ndipo mudzadya zonenepa za dzikoli.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa