Genesis 44:6 - Buku Lopatulika6 Ndipo anapeza iwo, nanena nao mau omwewo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20146 Ndipo anapeza iwo, nanena nao mau omwewo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa6 Wantchito uja ataŵapeza, adanena mau omwe adaamuuza aja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero6 Wantchito uja atawapeza ananena mawu anawuzidwa aja. Onani mutuwo |
Pakuti, taonani, ichi chomwe, chakuti mudamvetsedwa chisoni cha kwa Mulungu, khama lalikulu lanji chidalichita mwa inu, komanso chodzikonza, komanso mkwiyo, komanso mantha, komanso kukhumbitsa komanso changu, komanso kubwezera chilango! M'zonse munadzitsimikizira nokha kuti muli oyera mtima m'menemo.