Genesis 44:7 - Buku Lopatulika7 Nati kwa iye, Bwanji mbuyanga anena mau otere? Ngati nkutheka kuti akapolo anu achite chotero? Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20147 Nati kwa iye, Bwanji mbuyanga anena mau otere? Ngati nkutheka kuti akapolo anu achite chotero? Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa7 Iwo aja adamuyankha kuti, “Kodi mukulankhulazi nzotani bwana? Ife sitikadatha mpang'ono pomwe kuganiza kuti tichite zimene mukunenazi. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero7 Koma iwo anati kwa iye, “Kodi mbuye wanga mukuneneranji zimenezi? Sizingatheke ndi pangʼono pomwe kuti antchito anufe nʼkuchita zoterozo ayi! Onani mutuwo |