Genesis 44:5 - Buku Lopatulika5 Kodi si ndicho chomwera nacho mbuyanga, naombeza ula nacho? Mwachitira choipa pakutero. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20145 Kodi si ndicho chomwera nacho mbuyanga, naombeza ula nacho? Mwachitira choipa pakutero. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa5 Mwaberanji chikho chimene mbuyanga amamwera? Amati akafuna kudziŵa zam'tsogolo, amagwiritsa ntchito chikho chimenechi. Ndithu zimene mwachitazi nzoipa kwambiri.’ ” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero5 Mwaberanji chikho chimene mbuye wanga amamweramo ndi kugwiritsa ntchito akafuna kuwombeza? Chimene mwachitachi ndi chinthu choyipa.’ ” Onani mutuwo |