Genesis 44:2 - Buku Lopatulika2 Nuike chikho changa, chikho chasiliva chija, kukamwa kwa thumba la wamng'ono, pamodzi ndi ndalama za tirigu zake. Ndipo iye anachita monga mau ananena Yosefe. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20142 Nuike chikho changa, chikho chasiliva chija, kukamwa kwa thumba la wamng'ono, pamodzi ndi ndalama za tirigu zake. Ndipo iye anachita monga mau ananena Yosefe. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa2 Tsono pakamwa pa thumba la wamng'onoyo uikepo chikho changa chasiliva chija, pamodzi ndi ndalama zake zimene amati agulire tirigu.” Wantchitoyo adachita monga momwe adaamuuzira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero2 Tsono uyike chikho changa cha siliva chija, pakamwa pa thumba la wamngʼono kwambiriyu pamodzi ndi ndalama zake za chakudya” Ndipo iye anachita monga Yosefe ananenera. Onani mutuwo |