Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 44:3 - Buku Lopatulika

3 Pamene kudacha, anamukitsa anthu iwo ndi abulu ao.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

3 Pamene kudacha, anamukitsa anthu iwo ndi abulu ao.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

3 M'maŵa kutacha, anthu aja adaloledwa kupita pamodzi ndi abulu ao.

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

3 Mmawa kutacha anthu aja analoledwa kuti apite ndi abulu awo.

Onani mutuwo Koperani




Genesis 44:3
2 Mawu Ofanana  

Nuike chikho changa, chikho chasiliva chija, kukamwa kwa thumba la wamng'ono, pamodzi ndi ndalama za tirigu zake. Ndipo iye anachita monga mau ananena Yosefe.


Atatuluka m'mzinda asanamuke patali, Yosefe anati kwa tsanyumba wake, Tanyamuka, talondola anthu aja, ukawapeza unene nao, Chifukwa chanji mwabwezera zoipa m'malo mwa zabwino?


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa