Genesis 44:13 - Buku Lopatulika13 ndipo anang'amba zovala zao, nasenzetsa yense bulu wake, nabwera kumzinda. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201413 ndipo anang'amba zovala zao, nasenzetsa yense bulu wake, nabwera kumudzi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa13 Apo onsewo adang'amba zovala zao ndi chisoni. Adasenzetsanso abulu katundu wao uja, nabwerera kumzinda konkuja. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero13 Apo onse anangʼamba zovala zawo ndi chisoni. Ndipo anasenzetsa abulu katundu wawo nabwerera ku mzinda konkuja. Onani mutuwo |