Genesis 44:14 - Buku Lopatulika14 Yudanso ndi abale ake anadza kunyumba ya Yosefe; ndipo iye akali pamenepo; ndipo anagwa pansi patsogolo pake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201414 Yudanso ndi abale ake anadza kunyumba ya Yosefe; ndipo iye akali pamenepo; ndipo anagwa pansi patsogolo pake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa14 Yuda ndi abale ake atafika kunyumba kwa Yosefe, adampeza akadali momwemo ndipo onsewo adaŵerama pamaso pake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero14 Pamene Yuda ndi abale ake ankafika ku nyumba kwa Yosefe nʼkuti Yosefe akanali komweko. Ndipo anadzigwetsa pansi pamaso pake. Onani mutuwo |