Genesis 44:12 - Buku Lopatulika12 Ndipo iye anafunafuna kuyambira pa wamkulu naleka pa wamng'ono nachipeza chikho m'thumba la Benjamini: Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201412 Ndipo iye anafunafuna kuyambira pa wamkulu naleka pa wamng'ono nachipeza chikho m'thumba la Benjamini: Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa12 Wantchito wa Yosefe uja adafunafuna mosamala kwambiri kuyambira pa wamkulu mpaka pa wamng'ono, ndipo chikhocho adachipeza m'thumba la Benjamini. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero12 Kenaka anayamba kufufuza, kuyambira pa wamkulu mpaka pa wamngʼono. Ndipo chikhocho chinapezeka mʼthumba mwa Benjamini. Onani mutuwo |