Genesis 44:11 - Buku Lopatulika11 Ndipo anafulumira natsitsa pansi yense thumba lake, namasula yense thumba lake. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201411 Ndipo anafulumira natsitsa pansi yense thumba lake, namasula yense thumba lake. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa11 Motero onsewo adatsitsa msanga matumba ao, aliyense nkumasula thumba lake. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero11 Tsono onse anafulumira kutsitsa pansi aliyense thumba lake ndi kulitsekula. Onani mutuwo |