Biblia Todo Logo
Baibulo la pa intaneti
- Zotsatsa -




Genesis 44:10 - Buku Lopatulika

10 Ndipo iye anati, Tsononso chikhale monga mwa mau anu: iye amene ampeza nacho adzakhala kapolo wanga; ndipo inu mudzakhala opanda chifukwa.

Onani mutuwo Koperani

Chichewa Buku Lopatulika Bible 2014

10 Ndipo iye anati, Tsononso chikhale monga mwa mau anu: iye amene ampeza nacho adzakhala kapolo wanga; ndipo inu mudzakhala opanda chifukwa.

Onani mutuwo Koperani

Buku Loyera Catholic Edition - Chichewa

10 Apo wantchitoyo adati, “Chabwino. Komatu wina pakati panupa akapezeka ndi chikhocho, ameneyo akhala kapolo wanga, ena nonsenu muzipita mwaufulu.”

Onani mutuwo Koperani

Mawu a Mulungu mu Chichewa Chalero

10 Iye anati, “Chabwino, tsono zikhale monga mwaneneramu. Komatu aliyense amene angapezeke nacho chikhocho adzakhala kapolo wanga, ndipo ena nonsenu muzipita mwaufulu.”

Onani mutuwo Koperani




Genesis 44:10
6 Mawu Ofanana  

Ndipo anafulumira natsitsa pansi yense thumba lake, namasula yense thumba lake.


Ndipo iye anati, Ngati kutheka kuti ndichite chotero! Munthu amene anampeza nacho m'dzanja lake adzakhala kapolo wanga: koma inu, kazipitani ndi mtendere kwa atate wanu.


Tsopanotu, mtumiki wanu akhale kapolo wa mbuyanga m'malo mwa mnyamata; mnyamatayo akwere pamodzi ndi abale ake.


Iye wa akapolo anu ampeza nacho afe, ndipo ifenso tidzakhala akapolo a mbuyanga.


Litamtulukira dzuwa, pali chamwazi; wakubayo azilipa ndithu; ngati alibe kanthu, amgulitse pa umbala wake.


Titsatireni:

Zotsatsa


Zotsatsa