Genesis 44:9 - Buku Lopatulika9 Iye wa akapolo anu ampeza nacho afe, ndipo ifenso tidzakhala akapolo a mbuyanga. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 20149 Iye wa akapolo anu ampeza nacho afe, ndipo ifenso tidzakhala akapolo a mbuyanga. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa9 Tsono bwana, wina mwa ife akapezeka ndi chikho chimenechi, ndithu aphedwe, ndipo tonsefe tidzakhala akapolo anu, bwana!” Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero9 Ngati wantchito wanu wina pano atapezeka nacho chikhocho, ameneyo aphedwe ndipo ena tonsefe tidzakhala akapolo anu, mbuye wathu.” Onani mutuwo |