Genesis 43:26 - Buku Lopatulika26 Pamene Yosefe anadza kunyumba kwake, analowa nazo m'nyumba mphatso zinali m'manja mwao, namweramira iye pansi. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201426 Pamene Yosefe anadza kunyumba kwake, analowa nazo m'nyumba mphatso zinali m'manja mwao, namweramira iye pansi. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa26 Yosefe atabwera, abale akewo adapereka mphatso zija kwa iye, ndipo adamuweramira. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero26 Yosefe atafika ku nyumbako, iwo anapereka mphatso zija namuweramira pansi. Onani mutuwo |