Genesis 43:25 - Buku Lopatulika25 Ndipo anakonzeratu mphatso asanafike Yosefe usana; chifukwa anamva kuti adzadya chakudya pamenepo. Onani mutuwoChichewa Buku Lopatulika Bible 201425 Ndipo anakonzeratu mphatso asanafike Yosefe usana; chifukwa anamva kuti adzadya chakudya pamenepo. Onani mutuwoBuku Loyera Catholic Edition - Chichewa25 Tsono abalewo adakonzeratu mphatso zao zija kuti apereke kwa Yosefe masana, chifukwa anali atamva kuti akadya kumeneko. Onani mutuwoMawu a Mulungu mu Chichewa Chalero25 Abale aja anakonzeratu mphatso zawo zija kuti adzapereke kwa Yosefe, popeza anamva kuti Yosefe adzadya komweko masana. Onani mutuwo |